letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de pogona - sevenomore (mw)

Loading...

[intro]
yah
oh-yah-yah
oh-yah-yah
oh-yah-yah
oh-yah-yah

[chorus]
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona, gona
kunkonda pogona
amandifuna pogona, gona
kunfuna pogona

[verse]
k-mbali amandikana, amati ine ndine hule
k-mbali amandinyoza, ati ndine osauka
k-mbali amandikana, amangoti ndine mzake
k-mbali amandinyoza, ati ndimankakamila
koma zikamuvuta amabwera kwathu, “baby ine ndakusowa”
koma zikamuvuta amabwera kwathu, “baby ndili nawe nkhani”
komatu sakamba ayi, amangokhala pa easy
komatu sa-talker ayi, ndimangodziwa ma pg
ndimalakalaka nditabweza chipongwe koma ine zimandikanika
ndimalakalaka nditabweza choyipa koma ine zimandikanika
ndimamukonda ine, sindifuna atandisiya
ndimamufila ine, sindifuna ntamusiya
[chorus]
komabe, amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona, gona
kunkonda pogona
amandifuna pogona, gona
kunfuna pogona

[outro]
yah-yah, yah-yah
yah-yah, yah-yah
yah-yah, yah-yah
yah-yah, yah-yah, prr

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...