letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de udani - ndinezulu

Loading...

kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w-nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w-nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala

mwina ndi nyanga zomwe wina ana panga
kapena sinyanga nakuba kapena chabe nikaduka
kamene kalengesa banthu bamozi kupeza vif-kwa
cif-kwa mayeso fufuza koma sina peze cif-kwa eh
kunjako nko kudha macita mantha ndi khalidwe yawa
udani waconco wacoka kuti ma lankhulana
pempelo yanga niyoti izozo ma lalilane
nanga cikondi munali naco cinapita kuti
funso

kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w-nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w-nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala

k-makhalila midesu
ena akulila yesu
mundisamalile ana banja isa pwasuke tikhale ifeso
ogwilizana despite what we facing i hope we don’t break us ineo
pemphelo yanga ndiyoti udani ulipo kuntima uthepo
koma zukhala nga e sizotheka anthuwa afuna afepo
udani waconco ku opya ambuye k-mwamba muyanganilepo
k-ma kangana pa zopanda phindu poka poka ena afepo
anthu wa ndani aloza umbuli wa conci ine sina onepo

kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w-nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w-nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...