letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de chelele - molto zambia

Loading...

verse 1

ndinapti n’kasakile ma ganyu /
ku lusaka amai tionane/
ndi guleko ma bikiloni a new/
k-mudzi ugh! kulije money/
talema kudyela munkhwani, chambo, kachumbari ndi bonongwe /
mundi sungile bwino bulu langa, nondi pemphelela kukacha ngwee /
a mesiya az’ingo dutsa nane, kwa ine pomwe ndi saka money /
for his blessings to shower me mu nthawi ya mvula ndi sanane /
lekani kulila amai chete, conde musa sakamane /
am about to make the family proud ndikhulupirira musadande /
ndi londole, ndi bodole, za banja langa n’kuti /
ndi bwela ndi galimoto agogo zolima n’kulonga mubuti /
apo ndishi ndine mponda matiki taleka n’fuula njuchi /
nati ni ponye sitepe ni chinje zinthu pakuti /

chorus

amama alulila mabvuto achuluka aza cita bwanji ehh /
linagoma chimbira, tsono thonje akuti azalima bwanji ehh /
tsiku ndi caka, mwеzi ndi zaka ng’ombe nazo zingo buula ehh /
nda langa k-mwamba conde malipiliro apa mwеzi ndi machenji ehh /
ooooh conde amama musalile /
ooooh conde adada zaine /
ooooh conde agogo musalile /
ooooh conde abanja zaine /
verse 2

yeo amama kodi k-mudzi bwanji uko /
boma inawa ninkha atata fataleza uko /
chabwino k-mva koma nane ndili bho /
pepa ninali chete, zii sini napange call /
papita mwezi khumi lomba, ndi kungo joba, ena aona ndi zoba /
pa lusaka umoyo lomba, kucita soka, abanja ndikali lova /
ayi conde sizipopa, mutu wokoka, ndilu kankha ngati rover /
yehovah ndikalu konkha, kopanda ku oonjoka, tsiku lina aza sova /
mphaka tonse mbanja lathu tika bvale nsuti /
nthawi zonse ndima uza amai n’kuti /

bridge

tsiku lina ndi zadya ndi mfumu /
pa mbale imodzi sauce chi phumu /
kunena yesu ndinu m’kulu /
ku dutsa mo jeda-jeda conde ndikuti /

chorus

amama alulila mabvuto achuluka aza cita bwanji ehh /
linagoma chimbira, tsono thonje akuti azalima bwanji ehh /
tsiku ndi caka, mwezi ndi zaka ng’ombe nazo zingo buula ehh /
nda langa k-mwamba conde malipiliro apa mwezi ndi machenji ehh /
ooooh conde amama musalile /
ooooh conde adada zaine /
ooooh conde agogo musalile /
ooooh conde abanja zaine /

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...