letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de timalira(reggae version)[lawi cover] - mistah yemie

Loading...

[verse 1]
eeeii
eeeii

kodi wanyonga ndiye uti?
osak-mana ndimikwingwilima
njila yomwe onse amoyo
ayesedwa kulimba mtima

zochititsa mantha ena
zilimbitsa mtima ena
tifanana ndikusiyana
muzotipangitsa kulira
timalira mumtima
mong’ung’udza ndimo dandaura(ummmhh)
ululu ukasef-kira timaliraso mwa mkuwe(mayo!)

kulira kulibe mulingo
champweteka ndiye ayamba
sikuona nkhope kulira mayo
maso ndiye mboni

[hook]
poti tonse timalira(ummmhh)
zikawawa(ummmhh)
tikakhumudwa(ummmhh)
zikalemera(ummmhh)
zika chuluka
mutu ukakula usalewa nkhonya(mayo!)

timalira(ummmhh)
zikawawa(ummmhh)
tikakhumudwa(ummmhh)
zikalemera(ummmhh)
zika chuluka
mutu ukakula usalewa nkhonya(mayo!)

timalira mumtimamu
timalira monga ana
ndi misozi nayo
imakhara ikulakatika
timalira mumtimamu
mama mama(mama mama)
mama mamamamamama(ummmhh)
mayo!

[verse 2]
mtima uli nayo misozi
yosaoneka yongothera nkati
ndi misozi yosapuputika
mayo

woo oh
iwe tsambalanga kuwala mudzuwa
gwedera munphepo
kukongora kwako kosililitsa
kuli kunja ulira nkati

iwe tsambalanga
gwedera munphepo asazindikire
dziko likonda olimba mtima
mwananga

[hook]
poti tonse timalira(ummmhh)
zikawawa(ummmhh)
tikakhumudwa(ummmhh)
zikalemera(ummmhh)
zika chuluka
mutu ukakula usalewa nkhonya(mayo!)
timalira(ummmhh)
zikawawa(ummmhh)
tikakhumudwa(ummmhh)
zikalemera(ummmhh)
zika chuluka
mutu ukakula usalewa nkhonya(mayo!)

timalira mumtimamu
timalira monga ana
ndi misozi nayo
imakhara ikulakatika

timalira mumtimamu
mama mama(mama mama)
mama mamamamamama(ummmhh)
mayo!

[interlude]
mayo mayo mayo!(mamamamama!)
mayo mayo mayo!(mamamamama!)
mayo!(mayo!)
mayo!(mayo!)
mayo!(mayo!)

mamamamamamama!(mamamamama!)
mamamamamamama!(mamamamama!)
ayo!(ayo!)
ayo!(ayo!)
ayo!(ayo!)

[hook]
ndati tonse timalira(ummmhh)
zikawawa(ummmhh)
tikakhumudwa(ummmhh)
zikalemеra(ummmhh)
zika chuluka
mutu ukakula usalewa nkhonya(mayo!)

timalira(ummmhh)
zikawawa(ummmhh)
tikakhumudwa(ummmhh)
zikalemera(ummmhh)
zika chuluka
mutu ukakula usalеwa nkhonya(mayo!)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...