letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de chiyanjano - lucius banda

Loading...

[chorus]
oooh chiyanjano, chiyanjano
ndicha ntundu wanji?
oooh chiyanjano, chiyanjano
ch-nkandidabwitsa

[verse 1]
chiyanjano chanu chonde amalume
ndi gulu lanu ch-nkandidabwitsa
ufumu wanji wapa chiweniweni
nd-nkadziwa izi sizidzatha bwino
ubwezi wanji wosa dzuzulana
tikudana, tikutha anthu athu
jakisoni ochiritsa anthu
ndiyemweyo inu munkaphera anthu oh!

[chorus x2]

[verse 2]
lero muku[?] taganizani ndalama ndi za chani izi?
mano akatha musamaswe phale
mulekere wana apitilize kukazinga
chifundo chake chiribe malire
muk-mbukire mbala pa ntanda paja
ndalama mwabisazi mukanapatsa amphawi
mukanagula ufumu wa k-mwamba oh!

[chorus x2]

[verse 3]
malume zinthu zikamangoyenda bwino
zikavuta, zikavuta zimavutiratu
malume maudindo anachulukitsa
nd-nkadziwa mudzathera m’ndende
azakhali nawo kuuma ntima
munthu wa mayi koma m’maso muli gwa!
ndalama mwabisazi mukanapatsa amphawi
mukanagula ufumu wa k-mwamba oh!

[chorus x2]

[chorus x4]

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...