letra de yekha - jeg tellem
ye ye yeee
yeeeh
oh yeeeh tellem
aha yeah here we go
ndimafunitsitsa nditakhala wabwino
aliyense atamatengela ine
ndimafunitsitsa nditakhala chitsanzo
cholozeka pagulu la anthu
koma nthawi zambiri
ndimagwetsedwa mphwayi
chif-kwa cha zinthu zondizungulila
ndati nthawi zambiri
ndimabwezedwa mbuyo chif-kwa cha zochita za anthu ena
moyo w-nga aha
njira zanga izi
ndimafuna zizikhala za yehova yekha
thupi langa aha
ntchito zanga izi
ndimafuna ndizichita za yehova yekha
moyo w-nga aha
njira zanga izi
ndimafuna zizikhala za yehova yekha
thupi langa aha
ntchito zanga izi (izi)
ndimafuna ndizichita za yehova yekha
ndimafuna
njira zanga utasintha
ndimafuna
koma zimandikanika
ndimafuna
ndimafuna kukomana
ndimamuna
mamuna wa mtanda koma
koma ndikazamva za abusa
awapezelela ndi sister
nkhani ija ayiphiphilitsa
ine sizimandilimbikitsa ehe
ndikaona zophinja
sindichedwa ine kugiva
sindisilila u beliver
ndimaona ngati ndichedwa ehe
moyo w-nga aha
njira zanga izi
ndimafuna zizikhala za yehova yеkha
thupi langa aha
ntchito zanga izi
ndimafuna ndizichita za yehova yekha
moyo w-nga aha
njira zanga izi
ndimafuna zizikhala za yehova yеkha
thupi langa aha
ntchito zanga izi
ndimafuna ndizichita za yehova yekha
moyo w-nga aha
njira zanga izi
za yehova yekha
thupi langa aha
ntchito zanga izi za yehova yekha
za yehova yekha za yehova yekha
zizikhala za yehova yekha
za yehova yekha za yehova yekha
iye yesu
letras aleatórias
- trippythakid › letra de poppunksadhappyrapslapper - trippythakid
- massage music › letra de massage music - massage music
- bbq pope › letra de visions - bbq pope
- derby › letra de stop stalling - derby
- rap skillz › letra de random vs stoposto (title match) - rap skillz
- j killz › letra de rap god (cover version) - j-$killz
- slm california rapper › letra de westbound - slm (california rapper)
- neljansuora › letra de löytäjä saa pitää - neljänsuora
- yellow claw › letra de shotgun - radio edit - yellow claw
- cassettes wont listen › letra de kingdom - cassettes won't listen