letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de koma boys - crispy malawi

Loading...

[intro: crispy malawi]
koma boys
ayo nihilo bring the beat son haha
zomwe imapanga boys ina
isakuone ukuvina
koma ukulira
(hihihhihi)

[chorus: crispy malawi]
kundibela lighter ntakubanditsa(aah) (koma boys)
kundibela phone ntakuyakitsa(aah) (koma boys)
pamaso kuchiller k-mbali ku disser(aah) (koma boys)
kubwera pa den kundikalipitsa(aah) (koma boys)
tisamavetsana kuwawa
tizimvetsana kukoma boys
kuyikana mkati
osakankhirana mpaka ku khoma boys
k-magawanako wezi wezi
osamaphangira boys
slow paced kuvaya ku front
(tsitsa pang’ono)
osathamangira boys

[verse 1 :ace dirty & (crispy malawi)]
kundikweza kuzanditsitsa
mbiri yanga mumayipitsa
mumafuna zabwino zonse zikhale zanu
mukuwona moyo
k-mandiyenda mbali ngati nkhanu
k-mbali muku hater pamaso k-mandisamala
kufuna kulanda mkazi w-nga (koma boys)
kundiponda ka dollar kanga (koma boys)
osakapeza kamtima mumafuna zoyambana
pano ukupanga zanga
pano tinadana
[verse 2: krazie g & crispy malawi]
krazie tsitsi lako walitani?
ukubanda grade yanji?
ma trainer ngati njanji
ungobanda zi mbanji (zi m’banji)
kwa chigulu changa ine ndina lonjeza
tizingoyaka ku chaser ndi kombeza
kona drip yanga ikuteletele
tele tele
tele tele yeahhh
(koma boys)

[chorus: crispy malawi]
kundibela lighter ntakubanditsa (aah) (koma boys)
kundibela phone ntakuyakitsa (aah) (koma boys)
pamaso kuchiller k-mbali ku disser (koma boys)
kubwera pa den kundikalipitsa (aah) (koma boys)
tisamavetsana kuwawa
tizimvetsana kukoma boys
kuyikana mkati
osakankhirana mpaka ku khoma boys
k-magawanako wezi wezi
osamaphangira boys
slow paced kuvaya ku front
osathamangira boys
[outro: crispy malawi]
zomwe imayithoka boys
anyway osamaf–ka boys
[?]
kukakuponya ku falls
(zomwe imapanga boys ina)
(isakuone ukuvina)
(koma ukulira)
(koma boysss)
(koma boysss)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...