letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de mukunama - code sangala

Loading...

mukunama, mukunama,mukunama, mukunama
kodi ndi ndani ananene kuti onse oyimba ndi anthu osuta fodya
nanga ndi ndani ananena kuti onse oyimba amangomwa mkala bongo
mukunama, mukunama,mukunama, mukunama

tangoganizani moyo wanu ungakhale otani
patakhala panda nyimbo
manyado antundu onse amafika pa’nong’a akangothyolapo sound

mukunama, mukunama,mukunama, mukunama
mmm,acho,achi
acho,achi,acho,achi,acho,achi,acho,achi ugwi

mukunama, mukunama,mukunama, mukunama
eeh,sure
ajikandapasye
eehe,akulambusyatu walakwe
aaha,ugwi
aaha,ugwi
aaha,ugwi
aaha,ugwi,acho,achi
sure
yangali complain baba

mukunama, mukunama,mukunama, mukunama
mukunama, mukunama,mukunama, mukunama

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...