letra de ndi m'mene tiliri - yobezani
[intro]
classic
ace-tee on the beat
whoa! ine ndi thossa, uyu ndi yobezani
big tings ah gwaan, roll out, mvetselani
hip-op and dancehall, thoss dem talk
yoh, trap yuh ear, switch it on
[verse 1: huplex thossa]
mdalitso ndi w-nga n’naukwelera phiri
n’napempha sauzande wandipatsa milli
straight fram hustle chakhuminso ndi ichi
osadabwa iwe, ndi m’mene tiliri
yoh mi deh pan mi kneels yea, lord asante
mtima unasweka, mwati muumate
mi nuh fraid a none a dem, abwere sate
timayenda ndi tate
nde ayi sitibisa, nah
timapemphera, sitimakana
ukationa tikupambana
ndi m’mene tiliri, itsanana
yoh yobezani, ndi m’mene tiliri
ambuye ali likiliki
talking about god’s tings zilibe tikiti
go, go, go, go, go! thoss dem
[chorus]
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
[pan sunday inna church]
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
[sitimakhala ndi tense]
ndi m’mene tiliri [yah, yah, yah, yah]
ndi m’mene tiliri
[verse 2: yobezani]
i’m always vibing with my gang iwe taona
spirited up ngati sangoma
sizamatama man kungoti ndinaborna
sp-ce launched, dziko n’nadropper
ndine wake, anandisintha lifestyle
pondichitira chifundo ndili mu last mile
now i live for him mpake ndili agile
so i share hope, life yi ili fragile
sind-nkana, ndimam’tsata
olo dziko lindide bwanji
even atakhala sattah n’kupanga
zake zoti ndilidye banzi
ndili ndi bread of life, za njala ndinachotsa
ndinaiphula kale mpake ndima bosser
mfunse huplex, zin-z- tinat-ss-r
sinditengeka ’cause i roll with the most high
let’s go!
[chorus]
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
[pan sunday inna church]
ndi m’mene tiliri
ndi m’mene tiliri
[sitimakhala ndi tense]
ndi m’mene tiliri [yah, yah, yah, yah]
ndi m’mene tiliri
[outro]
so one mi jus buss dat
fi mi christ, big name, yuh jus know dat
yoh yobezani, tell dem, dem haffi know dat
yea, yea, yea, yea, yea, yea, know dat
[ace-tee on the b…]
yoh
ndi m’mene tiliri aise, yea
ndi m’mene tiliri
iwe madela
ndi m’mene tiliri
yea, yea, yea, yea, yea
letras aleatórias
- letra de la esquina - chino & nacho
- letra de buscando cabida - bhavi
- letra de incredible - lil bunna
- letra de animation - febueder
- letra de tuono - lil prodige
- letra de du kannst noch nicht gehn - juliane werding
- letra de $ide - jocstar
- letra de lëïth säë - öxxö xööx
- letra de r.i.p. - house of krazees
- letra de how we stay (album version) - leschea