letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de namwali - vin van

Loading...

vin van – namwali ft dmus tha sting

(chorus) vin van

kunena zoona unabadwatu namwali
poti mtima w-nga onse ndinapatsa iwe
ndzakupatsa love mmene ine ndingathele
mu mtima mw-nga monse munadzadza iwe

verse 1 vin van

kunja kwacha blanket langa ndatembenuza
kupita pa sink mkamwamu nkuchuka
nkhope kupuputa kuchosa thukuta
kutenga chakudya chinangwa chokukuta

kuyang’ana pa window ndaona ukudutsa
uyunso ndindani ndayamba kudzifunsa
kuopa kupusa mwina ghetto kupusa
paja amati safunsa anadya phula safunsa

mwina ndiwe girl wachikondi changa
yemwe adzasunge moyo w-nga
osamala ndikusunga mtima w-nga
no breaking the heart
nga nga nga
mwina ndiwe girl wachikondi changa
yemwe adzasunge moyo w-nga
osamala ndikusunga mtima w-nga
no breaking the heart
nga nga nga

(chorus) vin van

kunena zoona unabadwatu namwali
poti mtima w-nga onse ndinapatsa iwe
ndzakupatsa love mmene ine ndingathele
mu mtima mw-nga monsе munadzadza iwe

(verse 2) dmus tha sting

onе of the kind
controlling the system no naz
no lie you got me so high
no money no love
she gimme love no money can buy
i can’t lie

come closer – k-mbaya

i had to keep it private
you won’t go outta my budget
till i’m in a casket
my love will never die (ey)
i figured it out
without you i can live then what is life?
oh my god
love comes first but she does
with your love try lucky next time but i doubt
the future look so bright ndiwe yanga nyali
lemme plant the seed mother of my kids
ndiweyo amene udzakhale

i had to choose
it would be you i can’t miss chandamale
i love it when you give it all
you know it’s love all night till morning
love it when you give it all
you know it’s love all night till morning
till morning

back to the hook (sing along)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...