letra de mphete - tsar leo
[verse 1: tsar leo]
mtima w-nga unatenga ndiwe
mbewu zanga uzafetsa ndiwe
ndikulumbira i’ll be there till the end of days
i’ll never change, i swear no ways
mpaka kale nkhale nawe
you should know that i’m there for you
chikondi changa was meant for you
ndikuveke mphete, tiwawitse a miseche
[chorus: piksy]
usadzatope, usadzachoke
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika
usadzatope, usadzachoke
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika, yeah
[verse 2: piksy]
i can be a headache sometimes
ndiwe opilira, umandipilira baby, yeah-eh
anthu otiwona patali amandisilira, amakusilira baby yeah-eh
ndekha singakwanitse, ndatsala pati m’malize
you making it look so easy
kodi zifunika luso izi?
sindifuna wina ayi
ndifuna muyaya ndi tsiku lina lowonjezera kukhala nawe
[chorus: piksy]
usadzatope, usadzachoke
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika
usadzatope, usadzachoke
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika, yeah
[bridge: tsar leo]
ndikuveke mphete, mphete, mphete, mphete, mphete
ndikuveke mphete, mphete, mphete
ndikuveke mphete, mphete, mphete
[outro: piksy & tsar leo]
usadzatope, usadzachoke
(please don’t let go, please don’t let go)
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika
usadzatope, usadzachoke
(please don’t let go, please don’t let go)
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika, yeah
(please don’t, please don’t let go)
usadzatope, usadzachoke
(please don’t let go, please don’t let go)
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika
usadzatope, usadzachoke
‘cause ukadzandisiya ndidzabalalika, yeah
(chonde, please don’t let me go)
letras aleatórias
- letra de iv(iv) - nukan shaqir
- letra de carmesí - dolphsun
- letra de memories - raven & kreyn & uplink
- letra de o sol - arnaldo baptista
- letra de cold - traplord midas
- letra de irresponsable - memphis la blusera
- letra de bleed on - m67
- letra de ⚰️ serce ⚰️ - kodziak
- letra de one of a kind - camilla gulì
- letra de cabalgando hasta el infierno - meridiam