letra de ndalama - trappy beats
[chorus]
aseh trappy!
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndi zi nkhani (chif-kwa cha) (chif-kwa cha!) (chif-kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)

[verse 1]
maluzi ndatchekela
ulimi nnayesa kale
ku runner ma taxi
kuna ma tip
kusaka money tiguleko drip
ndalama ndalama ndalama ndalama satana
ndalama ndalama ndalama ndalama satana
kudzuka mma three ku den pita mma ten
osagona kusaka ma change
kudzuka mma three ku den pita mma ten
osagona kusaka ma change
ndaleka ndaleka zibwanazo ndaleka
ndatopa ndatopa eh zandicheka cheka
[chorus]
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndi zi nkhani (chif-kwa cha) (chif-kwa cha!) (chif-kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
misechе ndi zi nkhani (chif-kwa cha) (chif-kwa cha!) (chif-kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)
[verse 2]
yah yah
nkhani ndikunvana
nk-masaka ndalama yah yah
mpakana kudana kamba ka ndalama yah yah
nkhani ndikunvana
nk-masaka ndalama yah yah
yah yah
yah yah
maluzi maine
wandisiya mmalere
usandiuzе maine
ndikungosaka mandede
ndaleka ndaleka zibwanazo ndaleka
ndatopa ndatopa eh zandicheka cheka
[bridge]
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi
m’siye nzako
maluzi maluzi maluzi
maluzi maluzi maluzi
m’siye nzako
[pre-chorus]
ndakuthela ma plan(maluzi maluzi maluzi)(maluzi maluzi maluzi)
kodi nnalakwa chani (maluzi maluzi maluzi) (maluzi maluzi maluzi)
ndakuthela ma plan (maluzi maluzi maluzi) (maluzi maluzi maluzi)
kodi nnalakwa chani (maluzi maluzi maluzi) (maluzi maluzi maluzi)
ndalama ndalama
[chorus]
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndi zi nkhani (chif-kwa cha) (chif-kwa cha!) (chif-kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)
ndakuthela ma plan (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?) (ndipange bwanji?)
kodi nnalakwa chani? (kuchulusa) (kuchulusa) (kuchulusa)
miseche ndi zi nkhani (chif-kwa cha) (chif-kwa cha!) (chif-kwa cha!)
ndalama ndalama (aah aah ah)
letras aleatórias
- letra de suzie noma - mdq
- letra de sing it - emjay (ca)
- letra de gallo rojo, gallo negro - sílvia pérez cruz
- letra de já não sei - badoxa
- letra de stay lit - geminijynx
- letra de late night - lilwaterbed
- letra de la cleptomana - buena vista social club
- letra de heart in me - leaving thomas
- letra de what it is to burn (acoustic) - finch
- letra de stepsisters' lament - richard rodgers