letra de kwanu nkwanu - suffix (mwi)
[intro:]
listen
[verse 1:]
bambo anga ankandikhazika
pansi, ndili mwana wovuta
ndili chakusekondale heee ndisakuganizaso zoyimba
mwana w-nga ndithu kukula
ife taonapo yambili mvula
ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu k-manda
kusukulu komwe uliko, uzik-mbuka komwe uchokela
nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe -n-lowela
[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w-nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w-nga
dziwa dziwa mwana w-nga
dziwa dziwa, mwana w-nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga
heeehhh
[post-chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[verse 2:]
yea, life sikhala fair
macritisism sabweletsa sheda
aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela
k-masiyanitsa azako ndiabale
ena utavutika sangathandize m’bale
osamatengeka akamakuchemelera
enawo ukazazizila azakupanga chandamaleee
[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w-nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w-nga
dziwa dziwa mwana w-nga
dziwa dziwa, mwana w-nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga
heeehhh
[post-chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[outro:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w-nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w-nga
dziwa dziwa mwana w-nga
dziwa dziwa, mwana w-nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu
mwana w-nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w-nga
heeehhh
letras aleatórias
- letra de forró talaj - luke benz
- letra de no one knows about shekainah - days of january
- letra de isso fortalece - ana maria braga
- letra de all i ever wanted (face tat) feat. lil ac, dirty motrin - parish gunnar
- letra de skyrockets - jan terri
- letra de zequinha - éme (portugal)
- letra de feturing you - logan henderson and kendall scmidt
- letra de is today worth waking up for - hans gruber and the die hards
- letra de facile - veda
- letra de check - sunrey