letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de yesu amakukhala - shammah vocals

Loading...

mwina mavuto ak-mata
mwina matenda akukantha iwe ah
usade nkhawa ndimantha noah
ayesu amakukhala
usade nkhawa ndimantha noah
ayesu amakukhala
(x2)

he call you nkazi wapa bench
amakukonda when he’s broke koma
usalore divorce
by fire by force
yesu amakukhala mvera
usalore divorce
by fire by force
yesu amakukhala

anzako onse ma cash-gater
akuyendera hummer iwe zero mvera
usalowe ukachari
by fire by force
yesu amakukhala koma
usalowe ukachari
by fire by force
yesu amakukhala

mwina mavuto ak-mata
mwina matenda akukantha iwe ah
usade nkhawa ndimantha noah
ayesu amakukhala
usade nkhawa ndimantha noah
ayesu amakukhala

kukula aunti mukukula
mamuna banja sakupezekaa koma
usakhetse misonzi
by fire by force
yesu amakukhala mvera
usakhetse misonzi
by fire by force
yesu amakukhala

ndiwe born-again very hot
koma mwina fees ikusowa mvera
usayambe ukawalala
by fire by force
yesu amakukhala mvera
usayambe ukawalala
by fire by force
yesu amakukhala

(beat solo)

ayesu amakukhala
ayesu amakukhala

mwina mavuto ak-mata
mwina matenda akukantha iwe ah
usade nkhawa ndimantha noah
ayesu amakukhala
usade nkhawa ndimantha noah
ayesu amakukhala

usakhetse misonzi
by fire by force
yesu amakukhala mvera
usakhetse misonzi
usakhetse misonzi
by fire by force
yesu amakukhala

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...