letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de palowa njoka - sevenomore (mw)

Loading...

[pre-chorus]
yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
palowa njoka pano ndiye mkundifunano
dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
dzana dz-n-li munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)

[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka

[verse 1]
amakufuna zikakhalatu zawavuta (yah, yah, yah, yah)
yah, amakufuna zikakhalatu zawathina (yah)
yah, koma ku party umva asabwere amene aja ndachamba
koma ku ukwati umva asabwere amene aja ndamowa (oh my god)

[pre-chorus]
yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
palowa njoka pano ndiye mkundifunano
dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
dzana dz-n-li munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)
[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka

[verse 2]
yah, amafuna uzivutika
amafuna uzingopempha
amafuna uzisawuka
inenso ndekha ndisamapushe, yah, yah
pano p-n-lowa njoka
ka banja kajaso kanatha, p-n-lowa njoka (palowa njoka)

[chorus]
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka (palowa njoka)
palowa njoka
[outro]
yah, yah, yah, yah, yah
yah, yah, yah, yah, yah
panopa p-n-lowa njoka
p-n-lowa njoka
p-n-lowa njoka
p-n-lowa njoka
panopa p-n-lowa njoka
p-n-lowa njoka
p-n-lowa njoka
p-n-lowa njoka
p-n-lowa njoka
panopa p-n-lowa njoka, rr
yah, yachina seven adah

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...