letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de zima - sagonjah & tadala

Loading...

[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf–ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati

[verse 1: tadala]
sindikayika
kuli mtima wako sikutalika
minga yachikondi mayo mtimawu wabayika
nde umaona ngati ndimakusata mapazi
ndikadekha ndekha jenkha manyazi
phone sumandiyankha ndimafoka
ndimafuna pena k-mandikankha
umatalikira
umatayilira
olo namondwe panyanja amakalipira
umandipilira
kupangitsa zinthuzi k-mapitilira
vundula madzi akhoza k-madikira
ndiwe w-nga komabe mtimawu umakusilira
madzi ak-mwa osamapisilira
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf–ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati

[verse 2: sagonjah]
mwina ndi mantha chabe
simmawupeza ndisaname
mwina m’mangawa simnachile ndimilandu yatizibwezi takale
mwina ndi mamuna wansanje
mwina, mwina ndi trauma
chikondi chandiwonetsa zowawa
pano [?] kuteteza mtima w-nga
koma mai mai kalanga
muzitaye zonse ine mmapanga
siine m’ngelo pena ukali
kaduka kuswaya chikondi kutali
koma ngati tingak-mane pakati
tonse tikubwеla kuk-mana mkati
zomwe ndipeleka ndi zomwе ndiyembekeza
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf–ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje

[bridge]
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf–ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...