letra de umudziwe - sagonjah & tadala
(hook)sagonjah
umudziwe mulungu
pa wekha, pa wekha
umudziwe mulungu
pa nokha, pa nokha
(tadala)
mukachisi mwalowesa hustle
yesu chachikhumi abusa ka mphatso
pomwe ayimangilira
anzawo tikulira
si chamba nkafila maso
maonekedwe anga mumaziwa ku judger
one thing i know zonse amaziwa ndi jah jah
mumudziwe obadwila mu yudeya
njala sizamva azandiuza uyu deya
chipulumutso chikanakhala pa nsika
ma prophet ambiri ali ndi mavenda
munthu ndi munthu samayamika
yopanda khini nsanje ndi matenda
ndale ku guwa kuguwa nyanga
bola ndimudziwe mlengi mu mtima mw-nga
ntchito za mulungu palibe sungandipose
nkuseseleka ndi malamulo ngati mose
(bridge) sagonjah
umudziwe umudziwe
mulungu
umudziwe umudziwe
mulungu
umudziwe umudziwe
mulungu
umudziwe umudziwe
mulungu
umudziwe umudziwe
mulungu
umudziwe umudziwе
mulungu
umudziwe umudziwe
mulungu
umudziwe umudziwе
mulungu
letras aleatórias
- letra de alongside mr. hyde - the vegabonds
- letra de el perro poochie - salvit4
- letra de choppa - dayzu
- letra de addicted to nothingness - lil jiblet
- letra de the one that hurts - club beirut
- letra de get to know you - adam evans
- letra de skyzm - og frexzz
- letra de toxic love - bexley
- letra de die without love - lolene
- letra de hard to face - godsticks