letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de mubwere - ritaa

Loading...

ritaa mubwere lyrics

oh, sispence, oh oh oh
ritaa.. h-llo?

(verse 1)
munachoka kuti mukukasaka ndalama
mpaka lero simunabwelerenso
munachoka kutisiya ndi amai athu
koma simunabwelere..
simumatumizanso chithandizo kunyumba
koma zoti mukuchita bwino tik-mva
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik-mbukira

(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba..

(verse 2)
tinakula, otilera -n-li mai athu
kuvutika pamodzi ndi amai athu
komanso mutangopita
achimwene anatisiya
ana anu akungolira
chilichonse kuvutikira
phone yokha mukanatiimbira (h-llo?)
kalata yokha mukanatilembera (you know)
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik-mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba

(bridge)
ohh, mubwelere kunyumba
oh, oh , oh ..
mubwelere kunyumba

(chorus)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...