letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de nena - oti$ dean

Loading...

[verse 1]
yandipeza nkhani
akuti uk-mandiyenda m’mbali
is it why ukungomakhala busy
these days suk-mandipatsa nthawi yako
unkayimba ma foni, ma foni
umati where are you
baby come and see me
now i’m lonely, lonely
ndikamakufuna suk-mapezeka

[pre-chorus]
ngati ukukondanaso ndi munthu wina
let me know, ndidziwe
maybe chikondi changa chasiya kukoma
let me go, ndiyende
tisamangotaitsana nthawi ndiwuze
no don’t you lie, funa ndidziwe

[chorus]
mwina vuto ndi ine nena nena nena
ngati ukufuna ndichoke nena nena nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena
mwina vuto ndi iwe nena nena nena
kodi umandifunabe nena nena nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena nena
[verse 2]
ndakananga ndi ma frenzo
ambilimbili pamene ndima defender iweyo
molo mopanga za ineyo
ndinali busy kufinyika kupanga za iweyo
zoti ndimakukonda anthu amadziwa
daily ndimakuwonetsa
koma kwa azinzako akamafunsa uk-mandibisa

[pre-chorus]
ngati pali munthu wina
let me know, ndidziwe
maybe chikondi changa chasiya kukoma
let me go, ndiyende
tisamangotaitsana nthawi ndiwuze
no don’t you lie (no) funa ndidziwe

[chorus]
mwina vuto ndi ine nena nena nena
ngati ukufuna ndichoke nena nena nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena
mwina vuto ndi iwe nena nena nena
kodi umandifunabe nena nena nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena nena
nena nena (nena) nena (nena) nena nena

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...