letra de daily - oti$ dean
[verse 1]
mtima wakana kukhala chete
(chete, chete)
ndimafuna nditakuveka mphete
(mphete, mphete)
iwe ndi w-nga athu onse adziwe
(adziwe, adziwe)
chikondi changa pa iwe sindingabise
(sindingabise), bise (sindingabise)
yeah ey, mommy nkazi uja ndamupeza
daddy komwe muliko konzekani
ndikamakhalidwe, kotchena mavalidwe
ndipo pakamwa pake siimatha nkhani
baby baby, baby baby
ndimakusowa ine
baby baby, baby baby
[chorus]
ndikufuna ndizikuona daily, daily, daily
tinkhani tako tokoma tija ndizimva
daily daily daily
zimandiwaza umandipasa busy iweyo daily daily daily
only you daily daily daily, daily daily daily
[verse 2]
kani chikondi chimathaso kukoma chonchi
ngati ndinali pa ulendo
nafika mu dziko la nkaka ndi uchi
iwe ndine tithamange opanda tchuzi
one-two, one-two, mpaka finishi
umandikondabe olo ndili mmaluzi
ndikazaiphula uzizangotchena gucci, gucci
ah ah ah umandimvеsa kukoma ngati k-maloto
ah ah ah usanditalikile tabwela undigwile nkono
sunday to sat-rday kukhala osakuona iwе
ine ndakana toto
baby baby, (baby baby)
baby baby (baby)
[chorus]
ndikufuna ndizikuona daily, daily, daily
tinkhani tako tokoma tija ndizimva
daily daily daily
zimandiwaza umandipasa busy iweyo
daily daily daily
only you daily daily daily, daily daily daily
ndizikuona daily, daily, daily
tinkhani tako tokoma tija ndizimva
daily daily daily
zimandiwaza umandipasa busy iweyo
daily daily daily
only you daily daily daily
(daily daily daily)
daily daily daily
letras aleatórias
- letra de the car room - jay freshko
- letra de textmehowupheel - barz2real
- letra de till the end - djay kennedy
- letra de sswrap - arash
- letra de beautiful - damso
- letra de can't tell me nothing - tony cartel
- letra de monster - r. davis
- letra de some kind of wonderful - love songs
- letra de youth of the world - crucial youth
- letra de matestep - captain rogue - captain rogue