letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de panado - onesimus muzik

Loading...

panado panado yeah mmm ma headache yeah mmm eeh
panado panado mmm eeh
amakonda miseche
amakondwa munthu adzivutika
zochitika ngati siopemphera
daily daily busy ntopola
kubaya ma damage
kuupasa moyo w-nga challenge
machitidwe awo ngati judas
makhalidwe awo ngati njenjete eeh

amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditaphokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka
amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditaphokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka

ndi nsanje apatseni, panado panado
panado panado
amweko panado panado
panado anado
mutu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka mwina ndi nsanje
kaduka, mtima wachigawega
mutu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka, mtima wachigawega
samafuna ndiyendere njale
samakondwa ndikamadya money
zikandiyendera amakoka chibale
zikamandivuta andinyoza k-mbali
koma mulungu andichita balance, i relax
amamenya nkhondo nditakhala pansi
adani anga onse alemba m’madzi
samakondwa nane

amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditaphokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka
amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditaphokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka

ndi nsanje apatseni, panado panado
panado panado
amweko panado panado
panado panado
mutu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka mwina ndi nsanje
kaduka, mtima wachigawega
mutu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka, mtima wachigawega

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...