letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de nizakupanga ngozi - ngozi family

Loading...

pobwela pa nyumba panga uyenela ku nkala ndi ulemu
cif-kwa ngati ulibe ulemu nizakupanga ngozi
ine ndikonda antu a ulemu
cif-kwa ine niziba kucaya tu mambama twabwino

tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu

pobwela pa nyumba uyenela ku nkala ndi ulemu
cif-kwa bena sibafuna vo kambakamba
vo kambakamba vi leta pamulomo
cif-kwa bena baziba kuyasha tukopo twa ngozi

tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
peleka ulemu
bena bacaya ngozi yovuta
kukopo
[?]

tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu

pobwela pa nyumba panga uyenela ku nkala ndi ulemu
cif-kwa bena sibafuna vo kambakamba
vo kambakamba vi leta pamulomo
cif-kwa bena baziba kuyasha tukopo twa ngozi

tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu
tiza cita cani
kwa inu anzatu
kuti mupeleke ulemu kwanzanu

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...