
letra de atate - ngozi family
[verse 1]
popita ku nchito a ibala to siya
ndalama ya chakudya pa nyumba
ngati ba choka ku nchito
ba pitila to bar
balezela moba wa 10 kwacha
pobwela ku nyumba ati iwe mukazi w-nga
nipase vi nsima na vi ndiyo
amai nabo ati imwe mulibe ku siya ndalama ya chakudya pano pa nyumba
atete iwo a yamba to kalipa
avula ma jacket ati nizaku lungiza iwe
[chorus]
a-a-atate lekani k-menyana ndi akazi atu
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
[verse 2]
please atate lekani ku chita ndeu
ine sindifuna ku menya amai anga
popita ku nchita mosaibala ku siya
ndalama ya chakudya pa nyumba
chif-kwa ntau ina ana onse
azankala ndi njala pano pa nyumba
amai nabo akati ayanguleko imwe mwa yamba ku bachita ndeu
[chorus]
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
[intrumental]
[chorus]
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
a-a-atate lekani k-menyana ndi amai atu
letras aleatórias
- letra de galilei - deeay
- letra de mi sueño* - myke towers
- letra de phantom feelings - abigail barlow
- letra de birth: stripped - jason dhakal
- letra de feat* - myke towers
- letra de crawlin' - the marc tanner band
- letra de here and noun - da' t.r.u.t.h.
- letra de eco - agua florida
- letra de spaceships - young thug
- letra de lime - moise