letra de maury - namadingo
namadingo
k-mvetsetsana inde tinkamvetsetsana
ija inali true love, tinkakondana ah ah ah
zatsogolo lathu zidali mmanja mwake, mwa mulungu
koma yemwe adanena palibe chosatha
sadanane zonse zimatha ah ah
zimawawa palibe chamuyaya ah ah ah ah
maury adandisiya, maury adakwatiwa
ine zidandiwawa koma (ululu umatha ah ah ah)
pakapita nthawi ine (mabala achila ah ah ah)
maury adandisiya komabe (ululu umatha ah ah ah)
moyo goes on (mabala achila ah ah ah)
palibe chamuyaya
papita nthawi ine, maury atandisiya
maury adakwatiwa
atapita maury nalo dziko lilandikulira
mtima kupweteka nk-mangopirira (kupirira)
pagulu uk-mwetulira k-mbali ukusisima ukulira
maganizo kuk-mbuka momwe chikondi ch-nkakomera
simomwe mtima wako nawonso umawawira
kutopa ndi kulira maso ku fiila
kufuna kudzimangirira ah ah ah
koma ayi ayi uh huh
zonse zimatha mchimwene w-nga
palibe chosatha mchemwali w-nga
zimawawa komabe, ululu umatha ah ah ah
papita nthawi komabe, mabala achila ah ah ah
ine maury adandisiya, komabe ululu umatha ah ah ah
ndipo mabala achila ah ah ah
maury adandisiya, maury adakwatiwa (palibe chosata ah ah ah)
ndipo palibe chamuya ah ah ah
olo ndalama imatha, iwe kukhala mmaludzi
maudindo amatha, iwe kukhala n0body
olo maludzi amatha, mutaipedza bandulo
inu minyama imatha, iwe kupеdza madalitso
ungo limba mtima (moyo ndi choncho moyo oh oh oh)
tsiku lina udzachira (moyo ndi choncho moyo oh oh oh)
letras aleatórias
- letra de to voltando pra farra - henrique e juliano
- letra de whole wide world - waka flocka flame
- letra de mejor me quedo solo - allen king
- letra de yowwych - watermelon
- letra de não para (ao vivo) - anitta
- letra de the night time - extended mix - dash berlin
- letra de ein dealer zahlt bar - dcvdns
- letra de kaksoiselämää - pate mustajärvi
- letra de jack jones - wrighty
- letra de tempestades de sal - s.e.s.