
letra de kumpeta milombe - mufrika
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
kuzebenza tisebenza bwino
ndalama timapeza
koma potsilizira pake eeh!
tinali nao anzathu
tinali kuseka nao
tinali nao astikana
odsziba kusamba bwino
nanga lelo alikuti
ambuye mwatisiyiranji
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwsila alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwasila alumbwana
iyi nthenda niyoipa
ndiponso siyimasankha
imagwira aliyense
kuyambira kubana mpaka makolo
koma anyamata ndi astikana
nibame bakula maningi
nangatu tizakhala bwanji
popeza ndiye tsogoro
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
letras aleatórias
- letra de nada es para siempre (don candiani reggaeton remix) - luis fonsi
- letra de sportowiec - forsette
- letra de there is a savior - the worship initiative
- letra de 2x2 - august
- letra de down (live at woodstock '99, rome, new york, july 25, 1999) - jewel
- letra de slow time vultures - elephant micah
- letra de manos rotas - dellafuente & morad
- letra de down on christmas - elapid
- letra de obsessed - narickfominskiy
- letra de norma - say she she