letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de hustle yanga - mastol

Loading...

anamwedyoo…
chichi!
ag-yi vivite kwacha angasumile mayunizi
mmmh pangali baba, mbiyah gha kusausya kwedyinji….napepe!

verse 1

ndikusaka-saka nthaka yoti ndikataka-taka
ndisathe dzaka dzaka nsakupata ya utaka
ndudziwa pali danga, oti thukuta langa
lipinduleko nsanga nzingoshupikabe nanga?

geri sinnamalize ndimangodziwa abacus
koma kudzafa mphawi ndi vuto langa basi
magobo omwewa, anzanga anayiphula
tinkagawana zibwente pano akudya mula!

zanga zamawa zisiyane ndi za dzulo ka
tsoka, matembelero zonse zasuluka
mbuye mundidalitse polowa ndi potuluka
ndikadzala ngati bin nziwola zochuluka

bridge

pang’ono pang’ono sindikupanga za phuma
matuku-tuku tuku-tuku supeza zokoma
mfundo ndamanga ndamanga ndizitchuk-ma tchuk-ma
kuthamanga thamanga mpaka ndizapate chuma

pre-hoook

ntchito za manja anga nzakukuta
ndipo ndidzadya changa chi thukuta
zifumbi za umphawi ndikuzikuntha
chitsogolo chokha chokha ndizisuntha

hook

ambuye mukadalitsa
(hustle yanga)
pomwe pakulimba ndidutsa
(hustle yanga)
ndipo idzandipindulitsa
(hustle yanga, hustle yanga, hustle yanga)
ambuye mukadalitsa
(hustle yanga)
pomwe pakulimba ndidutsa
(hustle yanga)
ndipo idzandipindulitsa
(hustle yanga, hustle yanga, hustle yanga)

verse 2

ma betrayer akufuna ndiyende bear
koma angachitenji nzakhala billionaire
nde eya, ndakana k-mangobleya
ndikakhuta madeya
k-maseweretsa cheya
kuzikanda nk-mageya
ndikulimbikira hustle itsegule gate
nde sindigiver mpaka ndizagule jet
pempho,skabana iziyendabe straight
nane ndufuna bentley yopanda number plate
awa zinatheka nde ine ndilekelenji ulova
nzaugonjetsa, ndizagula range rover
adani onse amatida ngati nissan
nkazangoti ndayiphula ndizakubonisani

bridge

pang’ono pang’ono sindikupanga za phuma
matuku-tuku tuku-tuku supeza zokoma
mfundo ndamanga ndamanga ndizitchuk-ma tchuk-ma
kuthamanga thamanga mpaka ndizapate chuma

pre-hoook

ntchito za manja anga nzakukuta
ndipo ndidzadya changa chi thukuta
zifumbi za umphawi ndikuzikuntha
chitsogolo chokha chokha ndizisuntha

hook

ambuye mukadalitsa
(hustle yanga)
pomwe pakulimba ndidutsa
(hustle yanga)
ndipo idzandipindulitsa
(hustle yanga, hustle yanga, hustle yanga)
ambuye mukadalitsa
(hustle yanga)
pomwe pakulimba ndidutsa
(hustle yanga)
ndipo idzandipindulitsa
(hustle yanga, hustle yanga, hustle yanga)

verse 3

sindingagwire njakata pali ntaji nkutakata
ambuye akathangata ndi zolusa akakantha
madalitso adzadzadza mavutowa adzakata
akandifungata nanga oyipayoso angata?
vuto likaph-ka sikuti iye sang-yankheyi
ukaima naye palibe angakukankheyi
poti anati ’gwira ntchito ine ndiyika dzanja’
nde ma guy ma guy musadabwe ndikasanja

bridge

pachoko pachoko phuma nkhupanga yayi
ulakhasyi ungasanga nawo vyakunowa yayi
mfundo nakaka nakaka nipangenge votchuk-ma
kuchimbira-chimbira mpaka nisange chuma

pre-hoook

ntchito za manja anga nzakukuta
ndipo ndidzadya changa chi thukuta
zifumbi za umphawi ndikuzikuntha
chitsogolo chokha chokha ndizisuntha

hook

ambuye mukadalitsa
(hustle yanga)
pomwe pakulimba ndidutsa
(hustle yanga)
ndipo idzandipindulitsa
(hustle yanga, hustle yanga, hustle yanga)
ambuye mukadalitsa
(hustle yanga)
pomwe pakulimba ndidutsa
(hustle yanga)
ndipo idzandipindulitsa
(hustle yanga, hustle yanga, hustle yanga)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...