letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de anakonza - mastol

Loading...

-pre-hook-

kuwala kwako ngakhale dzuwa limayimika manja//
n’naponda potani kuti iweyo ukhale w-nga//
-n-lenga nyenyezi ndi dzuwa,ndi amene -n-lenga iwe//
ndifunitsitsa tikathere pa guwa,mtima w-nga watenga ndiwe//

-verse 1-

mtima w-nga unasweka zinatsala ndi zidutswa//
nde nkhani za chikondi ndimazileka zizidutsa//
sind-nkafuna olo k-mva n’nasanduka gonthi//
mu mtima munadzadza ndi milandu ngati khothi//

ena ankaunena mtima w-nga ati ndiwo-//
vuta kuwukonda mwina umafila aunt tiwo//
anzanga mmawashisha akafusa ngati ndiwo//
anapangitsa kuti ine ndizikhalabe single//

ntak-mana ndiwe dziko linayamba kuzuna//
anthu anadziwa mtumwi wapeza ka tsuna//
thupi losala-la ngati sadwala malungo//
she a catholic,mfana wa aroma moti nnafera fungo//

ndapezadi sindingachite makaniso//
mtimau mwatengadi sindingasinthe maganizo//
ndaona kuwala kwako nde ndavomereza sure//
olenga iwe -n-lengaso nyenyezi ndi dzuwa//

-pre-hook-

kuwala kwako ngakhale dzuwa limayimika manja//
n’naponda potani kuti iweyo ukhale w-nga//
-n-lenga nyenyezi ndi dzuwa,ndi amene -n-lenga iwe//
ndifunitsitsa tikathere pa guwa,mtima w-nga watenga ndiwe//

-hook-

na iwe anakonza
(na iwe anakonza)
s-n-lakwitse anakonza
(na iwe anakonza)
na iwe anakonza
(na iwe anakonza)
s-n-lakwitse anakonza
(na iwe anakonza)

-verse 2-

anakonza inuyo mami eeh ndi kadaulo//
ntchito anayigwira palibe dandaulo//
monga khristu akondera church mmau a paulo//
nane nzakukonda choncho kukusiya ndi malaulo//

ndi kokongoletsa nde chikondi ndikatapila//
musandivuwule mtima mwake ndikakamila//
structure ya fine ngati clay soil//
kubhebha sikuchepa olo asinthe hairstyle//

mmmh beiby nzakutengera ku nkopola//
kukusintha dzina udzakhala mayi topola//
tiye kwanu konko tikalipire ya lobola//
kutsimikiza kuti palibe ozandisomphola//

ndili nawe plan ma//
ndikaona maso ake othwanima//
(maso akewo)
tsemwe ndikudziwa kuti yemwe//
-n-lenga nyenyezi -n-lenga ndiwe wemwe//

-pre-hook-

kuwala kwako ngakhale dzuwa limayimika manja//
n’naponda potani kuti iweyo ukhale w-nga//
-n-lenga nyenyezi ndi dzuwa,ndi amene -n-lenga iwe//
ndifunitsitsa tikathere pa guwa,mtima w-nga watenga ndiwe//

-hook-

na iwe anakonza
(na iwe anakonza)
s-n-lakwitse anakonza
(na iwe anakonza)
na iwe anakonza
(na iwe anakonza)
s-n-lakwitse anakonza
(na iwe anakonza)

-bridge-

ine ndakonda iwe wekha//
kukusiya ndi zosatheka//
i swear there is n-body better//
yahweh anakonza iwe//

-pre-hook-

kuwala kwako ngakhale dzuwa limayimika manja//
n’naponda potani kuti iweyo ukhale w-nga//
-n-lenga nyenyezi ndi dzuwa,ndi amene -n-lenga iwe//
ndifunitsitsa tikathere pa guwa,mtima w-nga watenga ndiwe//

-hook-

na iwe anakonza beiby
(na iwe anakonza)
s-n-lakwitse anakonza
(na iwe anakonza)
na iwe anakonza
(na iwe anakonza)
s-n-lakwitse anakonza
(na iwe anakonza)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...