letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de chete chete - mashallo samilo

Loading...

chete chete lyrics
chorus
chete chete, sausa nyama
(sausa nyama)
chete chete, sausa nyama
(sausa nyama)
chete chete, sausa nyama
(sausa nyama)
chete chete, sausa nyama
(sausa nyama)
verse 1
ngati pali mvuto, tikambilane
ngati takondana, tiuzane
ngati wina walakwa, tizuzulane
ngati pali mvuto, tikambilane
ngati takondana, tiuzane
ngati wina walakwa, tizuzulane
(back to chorus)
verse 2
ngati pali thenda, tiuzane
ngati pali mvuto, tipeze njira
ngati palakwika, tipeze njira
ngati pali dima, tiwunikilane (x2)
(back to chorus)x2
outro
ahah! che mashallo! tiyenayo, hehehe!
osangokwiya ahahahah, tiyakhulane basi hehehe! eyi!
la latata lala tatatata lalatatatataa (chorus to fade)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...