letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de i'm so tired of you (tiny desk (home) concert) - malawi mouse boys

Loading...

[verse 1]
ndikakhala wosauka ineyo
satana iwe ayi ayi umandinena
koma mulunguyo akadalitsa ineyo
satana iwe ayi ayi umandinena

[chorus]
woyipa iwe
iwe satana iwe, iwe satana
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe
iwe-iwe, iwe, iwe-iwe
satana iwe, iwe satana
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

[verse 2]
wabweretsanso iwe mabodza padziko pano iwe
satana iwe, ayi-ayi ndatopa nawe
wabweretsanso iwe, mavuto padziko pano iwe
satana iwe ayi-ayi ndatopa nawe

[chorus]
woyipa iwe
satana iwe, iwe, satana iwe, iwe
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe
ayi-ayi, iwe
satana iwe, iwе satana
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

[verse 3]
wabwerеtsanso iwe, mabodza padziko pano iwe
satana iwe ayi-ayi ndatopa nawe
wabweretsanso iwe kusamvana padziko pano iwe
satana iwe ayi-ayi ndatopa nawe

[chorus]
woyipa iwe, iwe
satana iwe, satana iwe
ayi-ayi
ndatopa nawe

ayi-ayi, iwe
satana iwe, satana iwe
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

ayi-ayi, iwe
satana iwe, satana iwe
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

[verse 4]
wabweretsanso iwe mulili padziko pano iwe
satana iwe ayi-ayi ndatopa nawe
wabweretsanso iwe kaduka padziko pano iwe
satana iwe ayi-ayi ndatopa nawe

[chorus]
iwe-iwe, iwe
satana iwe, iwe satana

iwe-iwe, iwe
satana iwe, iwe satana
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

iwe-iwe, iwe
satana iwe, iwe satana
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

iwe-iwe, iwe
satana iwe, iwe satana
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

iwe-iwe, iwe
satana iwe, iwe satana
satana iwe, ayi-ayi
ndatopa nawe

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...