
letra de kape! - lil al
[intro]
yo 14 you got another one
ha, hahahaha
lil alzizizo
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif-kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk-manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
[verse 1]
belo sh-t ndungoweneka za mtika
ngati ndimamvana ndi rose wabho bho
koma ndi wa cash drip
kungofika pa malo aliyense akufuna andimenyetse sip
tungodripper wa mame sungatipeze tik-menya ma nip
zi ana zuziwa i’m him zungofuna zindidyetse lip
ndungokakisser nipple kenako ndikadye nipla
umaziwa yanga ija sindiphweketsa limbwa
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif-kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk-manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
[verse 2]
nda dropper kwambiri ma guy mu game akubanika
ma trapper a ulesi onse nde ndik-maliza
ngati ulibe dollar ndiwe artist wokanika
feature price ndima charger ngati ndikukaniza (yeah, yeah)
anandi b-tcherko kale nde sindimgawatenge serious
kungomubweleka rack munthu wayamba kusanduka mysterious
ha k-machenjera ma kape atha kubela
atandi slima phone ndinawoneka ngati mfana wopepera
but i didn’t care mix ndinali mu club, chi mwana chimandigwedezera
kenako chikundinong’oneza “big slime ndimaku hopera”
ukamuuza boyfriend wanyuowani atakudyera mkaladi
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif-kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk-manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
letras aleatórias
- letra de how - king swayzie
- letra de da - 2ndfam
- letra de munchee antics - rebel xd
- letra de lost dog - rey-nuh!
- letra de icaro (reload) - irama
- letra de vrais de vrais - tlf
- letra de show and tell - mike mozart
- letra de faded friends - jager bonham
- letra de can't stop the feeling (disco suckz remix) - justin timberlake
- letra de my muse - dropout