letra de mpinganjira talk - lil al, crispy malawi & krazie g
[intro : lil al]
blxck fyxh i wanna use it as a target
yeah, yeah, yeah, yeah,yeah, yeah
lil al huh!
ayy!
[chorus: lil al]
gang sang-yidutse palibepo njira
chaka chino dollar nde tizigwira hmm
ndungofila ngati mpinganjira (ayy)
ndungofila ngati mpinganjira
gang sumng-yidutse palibepo njira (ayy)
chaka chino dollar nde tizigwira (huh)
ndungofila ngati mpinganjira (ayy)
ndungofila ngati mpinganjira (ayy)
[post-chorus: lil al]
zamaluzi sindingapange relate
broke n-ggas imakonda kubwera ndi hate
[verse 1: jeff nyimbo]
ulibe ndrama izo ndi zako
osathoka ine si nzako, mwina mwake ukusokoneza
ukuwona ngati ndi ine koma si ineyo
ukamba za ndalama kuno sinkhani
ku chiller ndi ma beat ndipatse plan
[verse 2: crispy malawi]
kufuna kupanga dollar ngati mpinganjira
on the road to riches ine sindikusintha njira
ma punch ndungoyika ngati ndina dealer
you can lean on me ngati pillar hahaha
ngati ndi sekekekeke
kufuna cream ndi cakеkekeke
[verse 3: krazie g]
old school, nеw school sitinasekere
akufuna new sound ndiwapekere
pa mid ngati makelelelele
yeah i got a b-lls n-gga, lendewelele
[verse 4: kushizzo]
kushizzo! yeah!
okay dollar tizigwira mpaka ku tsamwa
tungosuta g’s, sticx ndamgulira fwaka
kuvaya ku stu ndima verse ngati ku scom
mpaka nzayiphule ngati mpinganjira thom
ndimangojama ya ine,ku pusher hustle ya ine
kuposter ndi gang ya ine, usapange za ine
shizzo from the dizzo ndabwera ndi lil al
amapanga zanga (huh) samapanga za-
[verse 5: boi sticx]
i got money on my mind
better pay me if you owe me ndikukakamira
chaka chino ndiyiphula zikatheka usadabwe
ndizingodya paper koma bola zisakuwawe
komwe kuli cash, ndipatse google maps
ndimakonda ku pusher dancehall koma ndimafila trap
better pay me before i dip
kubwera ndi ka sipi
a huh!
[chorus: lil al]
gang sang-yidutse palibepo njira
chaka chino dollar nde tizigwira (hmm)
ndungofila ngati mpinganjira (ayy)
ndungofila ngati mpinganjira
gang sumng-yidutse palibepo njira (ayy)
chaka chino dollar nde tizigwira (huh)
ndungofila ngati mpinganjira (ayy)
ndungofila ngati mpinganjira (ayy)
[post-chorus:lil al]
zamaluzi sindingapange relate
broke n-ggas imakonda kubwera ndi hate
[outro]
blxck fyxh i wanna use it as a target
letras aleatórias
- letra de john stulgate - wesley willis
- letra de il ponte - claudio lolli
- letra de miss asp's song - original cast of love in hate nation
- letra de over and out - the delays
- letra de shattered heart pt. 3 - the956devil
- letra de レッツすいかどろぼう (let's suika dorobo) - crystal kay
- letra de da hip hop way (wild flow remix) - wild wes
- letra de le petit minou - stage lacroix
- letra de demons and angels - primal fear
- letra de окраина (outskirts) - алла пугачева (alla pugacheva)