letra de chifundo nane - lawi
[intro]
ayy
chifundo nane
chifundo nane
oh, chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
mtima w-nga don’t you worry
everything is gonna be alright
[chorus]
ambuye ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
mtima w-nga sudera nkhawa
chif-kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w-nga sudera nkhawa (oh no)
chif-kwa ali ndi chifundo nane
[verse 1]
machimo anga ndi ambirimbiri osawerengeka ndipo
mutazindikira zamumtima mw-nga mukhoza k-mandisala
m-th- kufuna kundimangilira ndikundiponya mu m’ndende
ndizokoma kundiweruza, nzovuta kundimvetsetsa
ndiye amene anandipanga amandidziwa
zinsinsi zangazi pamaso pake ndizosabisika
koma ngakhale ndimachimwa iye andikondabe
amatsegura manja ake ndi kundik-mbatira
[chorus]
oh, ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nanе
mtima w-nga sudera nkhawa
chif-kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w-nga sudera nkhawa (oh no)
chif-kwa ali ndi chifundo nanе (oh, yeah)
[verse 2]
ayi-yayi-yayi
ayi, ndachoka kutali, moyo w-nga ndi umboni
wandimenyera nkhondo, ndangokhala chete
pomwe adani anga andik-mbira mitsinje
wandimangira mlatho, ndayenda powuma
wandifewetsera zolimba zanga
[chorus]
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ine mtima w-nga (sudera nkhawa chif-kwa ali ndi chifundo nane)
ine mtima w-nga (sudera nkhawa
chif-kwa ali ndi chifundo nane)
letras aleatórias
- letra de vasya sport - ap2eks
- letra de under dina kläder - amanda aasa
- letra de un'altra primavera - cristiana verardo
- letra de subelo (further up) - static & ben el - סטטיק ובן אל
- letra de black hole - flstudioguru
- letra de shot down - mip & yung marcus
- letra de la manteca (remix)* - diamante ayala
- letra de i like bananas (because they have no bones) - hoosier hot shots
- letra de só quero degustar - jeferson peixoto
- letra de funk flex interlude - obie trice