letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de zifukwa - kiosk (mw)

Loading...

[intro: starnel mon]
(welcome to year 2099)
aah papalala pala papalala (tiye, tiye, tiye)
muli ndi zif-kwa
muli ndi zi–
ooow (emb)
ooh am on my miracle height
(its thug records)

[verse 1: starnel mon]
she thinks that i don’t love her (she don’t really care)
she say ndimamuganizila nkangolota (bola chithe)
nanga pamene paja umatani (tani)
nanga unali naye uja ndi ndani (ndani)
ndikalakwitsa ndimapanga makani
usazapiteso ndakupanga barn
muli ndi zif-kwa sis (sis)
chikhala ndi zoona zikanatchuka sis (sis)
inu mumangovuta sis
ndikatelo amakwiya sis (sis)
nkhani yake jealous mkazi asandipatse bho (jealous)
amene uja ndi ndan (eva, jealous)
ndiye mumacheza chani (ah, jealous, jealous, yea)

[pre-chorus: kiosk]
you cannot come at my house jus to chat can’t you come to chill
mukangot high ku dm kw-nga ndimadziwa kuti
[chorus: starnel mon]
muli ndi zif-kwa (kwa)
f-kwa, f-kwa, f-kwa
muli ndi zif-kwa (kwa) f-kwa, f-kwa, f-kwa

[verse 2: kiosk]
yea akangot high ndimadziwa kut akufuna cash
i want this and that if you can never do it you don’t really love mе
aaah sukufuna chikondi sundinvetsa mwina ndiwe gonthi
bwanj umandi treatеr chonchi
ulibe nthaw yanga ngakhale uli ndi watch
so now know the gist all i ever wished was kuti uzindikonda mene ndilili
umabwela ndi zif-kwa zambili mbili nsayike mkazi pa status you like who is this
so now know the gist all i ever wished was kuti uzindikonda mene ndilili
umabwela ndi zif-kwa zambili mbili
nsayike mkazi pa status you like who is this, yea

[pre-chorus: kiosk]
you cannot come at my house jus’ to chat can’t you come to chill
mukangot high ku dm kw-nga ndimadziwa kuti

[chorus: starnel mon]
muli ndi zif-kwa (kwa)
f-kwa, f-kwa, f-kwa
muli ndi zif-kwa (kwa) f-kwa, f-kwa, f-kwa

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...