letra de waganiza bwanji - jeff nyimbo
[intro: jeff nyimbo]
it’s you that mega
okay
[chorus : jeff nyimbo & kushizzo]
waganiza bwanji? waganiza chani?
umapanga chan?i izi wapangiranji?
ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?
waganiza bwanji? waganiza chani?
umapanga chan?i izi wapangiranji?
ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe (kushizzo)
ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?
[verse 1 : kushizzo]
don’t stop living your life
tsogolo lili manja mwako uzik-mbukira
upeze njira uthane nazo zikachuluka
usasiyile panjira wachoka kutali k-mbuka,utanyamuka
unali ndi lotto limodzi ,kudzayangalira ma sister ndima bro’s
koma apa lero kusintha iwe ndi chani kodi?
kuyiwala zomwe timakambirana limodzi
choice ndi yako uzivaya kapena uyima pompa
wagwa pansi koma dzuka kakamira loto
moyo ndi kamodzi panga ganizo la bho
utha kuseka lero koma uzalira mtsogolo
[chorus : jeff nyimbo]
waganiza bwanji? waganiza chani?
umapanga chan?i izi wapangiranji?
ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?
waganiza bwanji? waganiza chani?
umapanga chan?i izi wapangiranji?
ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?
[verse 2: jeff nyimbo]
moyo ndiwophwеka umangofuna plan
ukadzadza denga uli ndi ukali
plan plan ndi plan osayisintha man
mkazi ndi mkazi amasintha man
-n-lipa nzako anagwetsedwa
-n-lipa pa nzako anachеperapo
ukhoza kukhala dolo koma usali dolo
usadikire kuti zikupeze pa mkono
uzizite wasnga bwino paliponse liwiro
k-makhala ndi nkhwiro kusaka kuli mpoto
kuti uchiphule kuchichotsa pa moto
k-malingalira patali tikuvaya konko
[chorus : jeff nyimbo]
waganiza bwanji? waganiza chani?
umapanga chan?i izi wapangiranji?
ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe? (it’s you that mega)
waganiza bwanji? waganiza chani?
umapanga chan?i izi wapangiranji?
ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?
letras aleatórias
- letra de brooklyn basement ii - sincerely collins
- letra de sad boy/sad girl - letdwn
- letra de domino - johnny rain
- letra de la volta buona - max pezzali
- letra de maintainin' - grip
- letra de eigentlich - zate & jack center
- letra de não interfere - killa weed gang
- letra de love in the air - gfriend
- letra de someone new - ilovefriday
- letra de día tras día - lorelei tarón