
letra de musalire - isaac liwotcha
“[verse]
ndidaona (zodabwitsa)
panthawi (yamavuto) oh mama
akuchikazi (adatenga)
katundu yense (ndi ana omwe) oh mama
bambo awo (akali moyo)
koma ana onse (adawalanda) oh mama
ana asowadi (chikondi)
akhalangati (akapolo) oh mama
“[verse]
mukadatenga (katundu yekha)
sichikanakhala (chovuta) oh mama
koma mwatenga (ndi ana omwe)
kuwaika mgulu (lakatundu) oh mama
ana w-nga ndithu (akuvutika)
pamene ine (ndilipo) oh mama
nthawi zonse (ndimangolira)
kulilira (ana w-nga) oh mama
“[chorus]
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
“[verse]
mbuye mverani (kulira kw-nga)
magazi anga (akuvutika) oh mama
mtima w-nga (umafuna)
nditamakhala (ndi ana w-nga) oh mama
koma poti (adandilanda)
ana w-nga (amangolira) oh mama
abambo wathu (ali kuti?)
inu agogo (mutipelekeze) oh mama
“[verse]
ana anga (mudzipemphera)
ambuye amamva (mapemphero) oh mama
musade nkhawa (ambuye alipo)
ndiye adziku (tetezani) oh mama
nthawi zonse (mukamalira)
mtima mw-nga (chisoni) oh mama
ndipempha mbuye (namalenga)
kuti aku (yang’aneni) oh mama
“[chorus]
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
letras aleatórias
- letra de l'alchimiste - luks_l_alchimiste
- letra de mr.gloomy - yerin baek
- letra de friday night heights - tayyga
- letra de so young - jonahdills
- letra de o hallelujah - phillip-michael scales
- letra de kipot ja kattilat - plutonium 74
- letra de yellow jack - ye banished privateers
- letra de final war - krusher
- letra de yoga - émile bilodeau
- letra de the start - big son (jonas gott)