letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de akondakitale - gwamba

Loading...

[intro: lawi]
yi, aye-iye-yah
aye-iye-yah

[chorus: lawi]
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje

ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi

[verse 1:gwamba]
aish, ndalama nde yavuta pa nyasa
daily fans k-mayisaka
sikuwona zoti ndiwe shasha
k-menya business basi k-mayitsatsa
nde mukapeza ka ndalama sister, chonde k-makagwiritsitsa
mukamagona nako kukafunditsa
kwachuluka mbava nde muzikabisa

[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w-ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 2: gwamba]
aish, conductor pokwera umati 100 ndangokhala pansi ukuti 120
aseh, osaziyamba zin-z-
muno sindichoka ngati sundipatsa change
wekha ukudziwa dollar ili pa minga
povaya kudedza pena kukwera njinga
umayesa ngati ukundiyimba
lero lonkha wandilira sindiyimva

[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w-ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi

[verse 3: gwamba]
aish, komanso yesu akufuna change mama
koma change akufuna iye si ndalama
akufunitsitsa inuyo makamaka mutasintha ndikuyamba k-mutsata
mapemphero ndi hustle ya uzimu
mukapusa tsiku lomaliza, no change
mapemphero ndi hustle ya uzimu
ukapusa tsiku lomaliza, no change
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w-ngondivuta ndi umphawi
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko change
inu ulendo w-nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...