letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de koma adha - danielz(asher d)

Loading...

koma adha lyrics
[intro]
koma adha
ndine asher daniel
h.a.i.g.a
koma adha

[pre-chorus]
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
usanyozere hustle yanga iwe
usanyozere hustle yanga iwe

[chorus]
koma adha
sikupusa uku
sikupusa uku
koma adha
si ufiti inu
si ufiti inu
koma adha

[verse 1]
koma adha
penapake zomwe mmapanga zimandidabwitsa
koma adha, magobo tikawapeza inu mumaphweketsa
koma adha
si ufiti inu, si ufiti inu
koma adha
mumatamba inu, mumatamba inu
koma adha
maluzi pa malawi afikapo ndithu
koma adha
chaka chino tilemera ndima hustle athuwa
koma adha
[pre-chorus]
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
usanyozere hustle yanga iwe
usanyozere hustle yanga iwe

[chorus]
koma adha
sikupusa uku
sikupusa uku
koma adha
si ufiti inu
si ufiti inu
koma adha

[verse 2]
tikagwira ka babe kabwino mumadana nafe
koma adha
tikapita ku mowa simugula inu mm
koma adha
ka dollar kanu mufuna muzagulirе nyumba
koma adha
mzungu kubwera ku flames k-mangoluzabe mm
koma adha
akuti flamеs ikusewera ngati bakha
koma adha
nde mwati nyimbo yang-yi siyabwino? nsanje mm
koma adha
[pre-chorus]
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
usanyozere hustle yanga iwe
usanyozere hustle yanga iwe

[chorus]
koma adha
sikupusa uku
sikupusa uku
koma adha
si ufiti inu
si ufiti inu
koma adha

[verse 3]
koma adha
tikadzalemera azizati takhwimira
koma adha
ndife afana odekha sitimadzipopa mm
koma adha
uk-mvera nyimboyi ukuona ngat ndikunama
koma adha
iwenso penapake suli bwino ukuseka
koma adha
[pre-chorus]
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
ati game yachema lero kuvuta
koma adha
usanyozere hustle yanga iwe
usanyozere hustle yanga iwe

[chorus]
koma adha
sikupusa uku
sikupusa uku
koma adha
si ufiti inu
si ufiti inu
koma adha

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...