letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de ndi abale athu - crispy malawi

Loading...

[intro]
mhaaahahahaha
malawian
yeah
265 (f-ck it bro)
spe
sound gawwd

[pre-chorus]
ena aku shophetsa ganja (ganja)
ena aku shophetsa fanta (fanta)
ena amagulitsa mpasha kukana k-mwa ice london (ice london)
bola gin ndi fwaka (fwaka)
nde uzikonda ku husser (hustle)
legal or illegal boma silingakupatse mpamba mphw-nga

[chorus]
a police ndi a bale athu
apolice ndi a bale athu
apolice ndi a bale athu
apolice (apolice) ndi a bale athu

[post chorus]
kupeza money ndi (ushasha)
ndine street smart (hustler)
with my self made (kwacha)
blessings kuno ndiku (mtaja )
kupeza money ndi (ushasha)
ndine street smart (hustler)
with my self made (kwacha)
blessings kuno ndiku (mtaja)
[verse 1]
40pin kuipanga ikhale 80pin
sizikufunika degree
ndiza straight can’t you see?
ungoika focus
umve zomwe ndikunen-z-
anthu ndi ama jelousy
uka ma chaser zi papеr zi
rule number one
bе yourself don’t try to be me
uka burner ka cannabis
kosala uzikabisa
be your plug
cut off your middle man
ma move amadhulisa
basi maluzi taakhaulitsa

[pre-chorus]
ena aku shophetsa ganja (ganja)
ena aku shophetsa fanta (fanta)
ena amagulitsa mpasha kukana k-mwa ice london (london)
bola gin ndi fwaka (fwaka)
nde uzikonda ku husser (hustle)
legal or illegal boma silingakupatse mpamba(ha ha) mphw-nga (ha)

[chorus]
apolice ndi a bale athu(athu)
apolice (apolice) ndi a bale athu (ndi abale athu)
apolice ndi a bale athu (ndi abale athu)
apolice (apolice) ndi a bale athu
[post chorus]
kupeza money ndi (ushasha)
ndine street smart (hustler)
with my self made (kwacha)
blessings kuno ndiku (mtaja )
kupeza money ndi (ushasha)
ndine street smart (hustler)
with my self made (kwacha)
blessings kuno ndiku (mtaja)

[verse 2]
kukonda ku woker figure ku hita g spot (g spot)
hustle imayamba aka hitta record (record)
iiih ukufuna beef ase eko t bone
ndafika ndi stainado wachika ku cicod
spe ndi king of the ghetto fredo ndi ghetto king kong
funa kupanga billi kuvutisa ku ding dong
nyimbo zolemba ku ma message pano ndima ringtone
ma verse angozaza funa ndipeze vepi ku synod
gist yako ipeze vep ine ndilibe nayo ntchito(ntchito)
she’s in my bed after iwe k-mutengera galitos
uma trappa ndima chick koma onunkha zitosi (sh-t)
ndili mmutu mwama diva ngati ribbon
ndangotulusa chida weapon

[pre-chorus]
ena aku shophetsa ganja (ganja)
ena aku shophetsa fanta (fanta)
ena amagulitsa mpasha kukana k-mwa ice london (ice london)
bola gin ndi fwaka (fwaka)
nde uzikonda ku husser (hustle)
legal or illegal boma silingakupatse mpamba mphw-nga
[chorus]
apolice (apolice) ndi a bale athu (ndi abale athu)
apolice (apolice) ndi a bale athu
apolice (apolice) ndi a bale athu (ndi abale athu)
apolice ndi a bale athu

[post chorus : crispy malawi & mario bros]
kupeza money ndi (ushasha)
ndine street smart (hustler)
with my self made (kwacha)
blessings kuno ndiku (mtaja )
kupeza money ndi (ushasha)
ndine street smart (hustler)
with my self made (kwacha)
blessings kuno ndiku (mtaja)

[outro]
mtaja
mtaja
kodi wagoma kapena wapeza ku mtaja
mtaja
mtaja
nditha ku doja

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...