letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de bodza - crispy malawi

Loading...

[intro]
cheo meek
(kukonda ma bodza)
(umakonda ma bodza)(iwe)
(kukonda ma bodza)
(umakonda ma bodza)(ine)
(kukonda ma bodza)
(umakonda ma bodza)(ife)

[chorus: crispy malawi]
numbers don’t lie koma (bodza ndi labho)
sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho)
wapulumuka kangati ase(ndibodza lakolo)
kusekelela za bodza koma kukwiya ndi chilungamo(ndi chilungamo)
iwe numbers don’t lie koma (bodza ndi labho)
sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho)
wapulumuka kangati iweyo
kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (ndi chilungamo)

[verse 1:crispy malawi]
i wish you more life ndi zi good health
bodza ndi la bho koma don’t lie to yourself
titalke ma facts bwanji apa uwone ulire
practice makes perfect sunganame usana chalire
wamenya call ku vephi kuti sukufika bho
ukunama
mesa umangofuna ku chilla ndi boys
out here asking for the truth
koma you already know
kuti bodza laku saver wa dodger chilungamo
pa city pa dzadza ma bodza(bodza)
ma dolo kunamiza ma zoba(zoba)
akunama kuti aku baller(baller)
koma ali padеn kungopola(bodza)
koma akuzinamiza okha
ife trap ili makola
(ife you love mе)babe chilungamo pena chimazakola
pena ndimazanama kuti ulipo wekha
[chorus]
(bodza ndi labho)
sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho)
wapulumuka kangati ase(ndibodza lakolo)
kusekelela za bodza koma kukwiya ndi chilungamo(ndi chilungamo)
iwe numbers don’t lie koma (bodza ndi labho)
sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho)
wapulumuka kangati iweyo
kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (ndi chilungamo)

[verse 2: virus infectious]
(infectious) ati i love you
ndili ndi cash a ma bodza a bho
akazi onsewa nda bonzapo
afana ofewa cap ngati wavala chipewa
koma boys ati ndaba disposable
ndikuchita kusowa response ya bho
olo jokes pa mikozi po
ati dende the boys get toasted
roasting beats and beef
of course and some shots been dropping
see the way we run the streets
they dropping off like leaf we smoke them
got me coughing
some go deep like the ocean we floating [?]
you know what it is the clan is chosen bro
[outro: crispy malawi]
don’t lie koma(let’s go)
sindikunamizani guys koma(let’s go)
wapulumuka kangati ase(ndi bodza lako)
kusekelela za bodza (ndi chilungamo )

iwe numbers don’t lie koma
sindikunamizani guys koma
wapulumuka kangati iweyo(ndi bodza lako)
kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo(ndi chilungamo)

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...