letra de ayi zikomo - crispy malawi
[intro]
malawian
ayi zikomo
[chorus]
kudzuka mornaz kugwada pansi kuthokoza jah, jah f-kwa leronso ndadzuka ndi moyo
gratitude is a must ndimawinner ndikangodzuka sindimgaphwekese
ayi zikomo, ayi zikomo
yeah, ayi zikomo
[verse]
sorry ngati zili zapa easy kwa iweyo
kwa ifeyo ndiza hard takulira mu zikh0m-
kwachoka nzako pali malo ngati suk-mvesa ndekuti sunabholeko za after domo
ndimayenda ndi gang koma nditha kuyenda ndekha
ngati pomwe pali abalepo adani ali pomwepo
eish, funa imali wamva? ngati zili zosakhudza cash
zisandikhudze ndakana nono
dollar ya show sikukwana koma umakwana
no thanks, i can’t take the offer, ayi zikomo
i can’t show up at your place f-kwa ukufila ngati aliyense akuyenera ashale konko
mamva zomwe mandi mandinena ndimafuna kuyankha
koma ndikango burner ndimangoti (ayi zikomo)
[chorus]
kudzuka mornaz kugwada pansi kuthokoza jah, jah f-kwa leronso ndadzuka ndi moyo
gratitude is a must ndimawinner ndikangodzuka sindimgaphwekese
ayi zikomo, ayi zikomo
yeah, ayi zikomo
[outro]
zikomo, zikomo, ayi zikomo
letras aleatórias
- letra de 1994 rocketship - byemilo
- letra de bota pra girar - kalli (br)
- letra de cattle mutilation theories - father guido sarducci
- letra de no love - zay kenne
- letra de my jue, delilah - marvinkann
- letra de the hotspot - pacmantv, workrate & la f
- letra de no somos iguales - babi
- letra de sick - elijah kealy
- letra de gonna have some fun tonight - etta james
- letra de jason pirulo - some1 (esp)