
letra de angobwerabe - crispy malawi
[intro]
f-f9ine
[pre-chorus]
ma babe ambiri man angobwerabe
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik-mane
sitik-mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
[verse 1]
nnamukwera kale sanganditsike
ati ali ndi guy oti sangamu cheaty
ex w-nga wina anagwidwa ndi dj
koma ntafuna nditha k-mu caller kuti ndimu-
k-mudeleter ngati amangooneka bho pa ma pictures
ama roller ndi adani k-mawauza kuti andidisse
nnangoziwa kuti si level basi k-mandipanga compare ineyo ndi achina piksy
iwe, yachina spe ndi 1 of 1 sungamafananize
sindingakunamize, ngati sufila dancehal sindingakukakamize
nditha kushala nawe koma sindingakhalitse
umuuzenso blesser wako ndikugulisa ma lipha ndi ma t shirt
osamaphwеkesa mission
[pre-chorus]
ma babe ambiri man angobwerabе
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik-mane
sitik-mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
letras aleatórias
- letra de el chupetón - bronco
- letra de capitan - алла пугачева (alla pugacheva)
- letra de right place, wrong time - tom jones
- letra de la source - lili boulanger
- letra de it don't matter to the sun - matthew morrison
- letra de right to my head - marc copely
- letra de omie wise - okkervil river
- letra de conversations - eva gardner
- letra de ystävälle - jamppa tuominen
- letra de you're not play love - the wilburn brothers