letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de titani apa? - crispy malawi & horus dem bad

Loading...

[intro: crispy malawi]
eh, yeah, titani apa?
horus dem bad
titanana?
yeah, titani apa?
hm, titanana?

[chorus: crispy malawi]
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana

[verse 1: em-el, crispymalawi, bumoff]
kwatulukira chak-mwa
omwe anakhala chete ayamba kuyankhula
ma babe ayaka angowoneka zolawula
“can you escort me to the bathroom?” konko kupakula
nali busy kuchipatsa plan chimwana
apa ndakhansula after zitandibanda
big slime iwe njoka simayenda ndi ana
tikuyabwa ndife tiyangane akukanda
ay, ay
whiskey, whiskey, tisipitse whiskey
nde ma cheese angozungulira ngati disc
gang yanga yadzadza ma biggie
utha kusankha modzi kuti ujambule naye pic
[chorus: crispy malawi]
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana
nde apa tak-mana
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana

[verse 2: brainlock t-kas]
yeah
utha kuyambitsa plan ngati ukusonkha 40%
sitiku slimana apa macheza abhebhe
ndikasonkha njale sindisonkhaso ya baby
perfect day yoti babe yawinawake idyedwe
regular sunday nde ti trape apa
tifika monday ine zaku vepi mayaz
uhuh ndi anzanga tikupanga zoyaka ku promoter ma ganja

[chorus: crispymalawi]
titanana?
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana
nde apa tak-mana
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana
[verse 3: krazie g]
mh, titani lero? tibanditsane ma cheesaro
pabwere baby gin folo
palibe shot, tizingomwera mu botolo
lalata, malala mavuto onse kuyiwala [?]
konda kutchera simisala osamayiwala sine mfana ofwala
still focused on zigoli yeah, kusa ipoli [?]
ndamu caller boliboli ati ndi trape ma kush chapa chiboliboli
i got it now, i’m jolly and i got a few grams
in the bar i’m with three ships, we gon drink till we sick
dressed in a’ba.lé pink
pa 24 ndima droppa olo ndisagawe link
sloppy top when i’m coming is what she think
ndima runner dancehall, kuyambira sunday mpakana sunday
kupewa chibwana ndinasanduka chibwana
nde usandichedwetse honey ndukalinke ndi gang ndiuchape

[chorus: crispy malawi]
titanana?
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana, hm, okay
titani apa? eh? titani apa?
tipange za ma baby gin ndi zachamba
tisonkhe ma kitty, kitty tigule chak-mwa
ndi zomwe timapanga tikak-mana
[outro: crispy malawi]
titani apa? eh? titani apa?
kudzuka monaz tangowunyapa

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...