
letra de wakuba (interlude) - crispy malawi & dirty flo
[intro: dirty flo]
aku recorder ndi yashie
iwe aku recorder ndi yashie
iwe aku recoder ndi yashie
[pre-chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak-mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k-muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
[verse: crispy malawi & dirty flo]
k-mu caller dirty ati iyeyo ali kwa duda
kuyithoka boys yanga ati samasuta
koma amazanditenga kuvaya kwa plug koma kusonkha yamafuta
ndimadya ndine koma kungoti ghetto simakhuta
malo si ake koma ndadabwa wamasuka
attention yanga sinduyiwona ndani wasunga? (yeah)
atha kubela mpweya iwe ndikubanika
ofunika k-mu searcher uyu akamapita (mh)
(yeah, yeah) nde akamavina mpamene umaziwa kuti ass yangodzadza ndi ma fats
amangokwiya ati ndimachulutsa ma facts
pa tiktok ndimafila f-kwa ali ndi chi nyash
olo mbina ndamudabwa mene wanyamulira
waba uku koma uku nkomwe wajudukira
timuphika f-kwa watibela chopakulira
waba moto fanzi ikuwona ngati wazimitsira
[pre-chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak-mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k-muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
letras aleatórias
- letra de héros - ol' kainry
- letra de 12 3 - mutekii
- letra de haze - marlow ray
- letra de generation - lou christie
- letra de zaboravi me - vesna zmijanac
- letra de troubled childd - mudrigo
- letra de playdate - ajantha
- letra de dandelion wish - vanity mirror
- letra de leash* - brennan savage
- letra de fer en plastique - lets go