letra de miyala - cozizwa
intro
hey
hey heeeyah aye
heeeyah aye
verse 1
pakamwa pomwe ndiimbira nyimbo yanga
tsiku lina ndithu yahwe adzandifunsa (funsa x3)
pakamwa n’nakupatsa
n’chif-kwa chani unkaphyozera zingombingo?
miyendo yomwe uvinira nyimbo yang-yi
tsiku lina ndithu yahwe adzakufunsa (funsa x3)
miyendo nnakupatsa
ona unkapalasila kokabera anthu?
koma ine, koma ine
ine ndinsembe yamatamando
koma ine, koma ine
ine ndinsembe yamatamando
chorus
musandiuze ndikhale phee
apo bii miyala isokosa (miyala isokosa)
eeeeh sindikhala phee
apo bii miyala isokosa pano (miyala isokosa)
ndikuti shaa miyala isokosa pano (miyala isokosa)
isokosa pano (miyala isokosa)
ndikuti eeh miyala isokosa pano (miyala isokosa)
isokosa pano (miyala isokosa)
ndikuti shaa miyala ilalata pano (miyala ilalata)
ilalata pano (miyala ilalata)
ndikuti woh miyala ilalata pano (miyala ilalata)
miyala ilalata pano (miyala ilalata)
bridge
heey
kuli achina mbuzi
kuli achina ng’ombe
kuli achina makoswe
kuli achina mbalame
kuli achina mphaka
kuli achina agalu
kuli achina ntchentche
kuli achina ngumbi
verse 2
ine ndimachita chidwi ndi mwala
poti mwala ulibe pakamwa
koma kudzaiyang’ana mbuzi, ili kukamwa yasa
koma nkadzamuyang’ana galu, naye alikukamwa yasa (eeeh)
kudzaiyang’ana mbewa, nayo ili kukamwa yasamuleni
koma ngati mau akunena, mwala udzaimba nyimbo kuli bwanji makoswe
ngati mau akunena, mwala udzaimba nyimbo kuli bwanji mbewa
chorus 2
musandiuze ndikhale phee
inu apo bii miyala isokosa (miyala isokosa)
eeeeh ndati sindikhala phee
apo bii miyala isokosa pano (miyala isokosa)
ndikuti woh miyala isokosa pano (miyala isokosa)
miyala isokosa pano (miyala isokosa)
ndikuti woh miyala isokosa pano (miyala isokosa)
miyala isokosa pano (miyala isokosa)
ndikuti shaa miyala iyankhula pano
miyala iyankhula pano
ehhh miyala ichezapo pano
miyala ichezapo pano
ndikuti woh miyala ilalata pano (miyala ilalata)
miyala ilalata pano (miyala ilalata)
miyala ilalata pano (miyala ilalata)
miyala ilalata pano (miyala ilalata)
kuli achina mbewa
kuli achina nkhuku
kuli achina mphemvu
kuli achina gwafa
kuli achina mbatata
kuli achina khoswe
kuli achina nkhuku
outro
eh ine ndimtama tsiku lonse
ndimtama tsiku lonse ineyo
ndati ndimtama tsiku lonse
ine ndimtama tsiku lonse
ndimtama tsiku lonse
ndimtama tsiku lonse
eeeeh ndati ndimtama tsiku lonse
ine ndimtama tsiku lonse
letras aleatórias
- letra de russian hotel aftermath - emmure
- letra de pilu - galuh
- letra de cóncavo y convexo - la rosa
- letra de шагане - гуджа бурдули
- letra de rejoice in the richmondd - sanjeev enos masih
- letra de blindfolded (reprise) - simple minds
- letra de simple girl - girls' sample
- letra de us - uss (ubiquitous synergy seeker)
- letra de насдвое - курара
- letra de campfire! - 칵스