letra de ndipunziseni - chiyembekezo music
chiyembekezo – ndiphunziseni (lyrics)
(female intro)
koma ndinena muyende yende ndimzimu ndipo misafise chilakolako chathupi x2
[this i say walk in the spirit and do not fulfil the l-st of the flesh]
(verse 1 – solo)
ndipo nchito zathupi zionekela abale ndizo dama, chodetsa, kukhumba zonyansa, kupemveza mafano nyanga, madano, ndeo kaduka, zo’optsya m’tima, zotetana, magawano, mipatuko, njilu, kulezela m’chezo, ndizina zotele abale
[for the works of the flesh are evident that is adultery, formication, uncleanness, idolatry, witchcraft, hatred, variance, emulations, wrath, strife, sedition, heresies, envying, drunkenness, revellings and as such like….]
(chorus – females)
pakuti thupi lilakalaka potsutsana naye m’zimu, ndi m’zimu potsutsana nalo thupi x2
[for the flesh l-sts against the spirit and the spirit against the flesh]
(verse 2 – solo)
ndiphunziseni chikondi
ndiphunziseni chimwemwe, ndiphunziseni mtendere, kuleza m’tima, kukoma m’tima, kufeba m’tima, chikhulupililo, chifaso, chileso. (females) “popanda zimenezi palibe lamulo ouo ououo ououo.”
[teach me love, joy, peace, patience, kindness, goodness, faithfulness, gentleness, self-control, (females) “against such there is no law ouo..ououo ououo.”]
(chorus – females)
pakuti thupi lilakalaka potsutsana naye m’zimu, ndi m’zimu potsutsana nalo thupi x2 [for the flesh l-sts against the spirit and the spirit against the flesh]
(hook)
ngati tili ndimoyo ndim’zimu (ndim’zimunso tiyende)
tisakhale ozikhuza outsana akuchitilana njilu, njiluuuu
[if we live in the spirit, let us also walk in the spirit. not be desirous of vain glory, provoking one another, envying one another]
(chorus – females)
pakuti thupi lilakalaka potsutsana naye m’zimu, ndi m’zimu potsutsana nalo thupi x2 [for the flesh l-sts against the spirit and the spirit against the flesh]
letras aleatórias
- letra de có còn yêu nhau - (vok) john
- letra de 10 mln - zame
- letra de interference - sect (hardcore)
- letra de grave situation - black absence
- letra de lubin feat. sparrow - banita - lubin & sparrow
- letra de mañana - roger clyne & the peacemakers
- letra de brightest days - cancer bats
- letra de stasis - vctms
- letra de blackbook vinculo - hablando en plata squad
- letra de cry for you (single edit) - september