letra de kunditaya - alick macheso
[intro: jonas kasamba]
al!ck macheso, agitate of sungura, atomic bomba
[verse 1: al!ck macheso]
abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii
ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii w-nga oooo
[verse 2: al!ck macheso]
kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
kunditaya, kunditaya, kunditayira mudzenje abambo anga ine ndithu
kunditaya, kunditaya, kunditayira muchitini abambo anga ine ndithu
[verse 3: al!ck macheso]
kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
[chorus: al!ck macheso]
abambo anga ine (abambo anga ine), umoyo w-nga ine (umoyo w-nga ine), wokulira muumphawi (wokulira muumphawi), ndine mwana wa masiye ine (ndine mwana wa masiye ine)
zomvetsa chisoni, ndithu siumoyo wosangalatsaa
[outro: al!ck macheso]
ndilibe chomwe ndingapange ineyo chif-kwa ndine mwana
chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
(abambo anga inee ndithu)
ndilibe chomwe ndingapange ineyo chif-kwa ndine mwana
chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
letras aleatórias
- letra de pro patria suite - strawbs
- letra de without technology - no wrong numbers
- letra de walked in (freestyle) - cjay
- letra de who i am - james mcvey
- letra de burden - hoops
- letra de exit the void - grim singmuf
- letra de all around me - lange
- letra de doses de amor - mob79
- letra de mach dich nützlich - k.i.z.
- letra de 1 red shell - wiley