letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de impfa nimulandi - alick macheso

Loading...

[intro: jonas kasamba]
yeeeeeeh! chesology!

[chorus: al!ck macheso]
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga amayo

[verse 1: al!ck macheso]
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w-nga, -n-li wachikondi
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w-nga, -n-li wachikondi mayo

[verse 2: al!ck macheso]
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda achibwenzi wathu
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda anzanga, achibale amayo

[verse 3: al!ck macheso]
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe amayo

[verse 4: al!ck macheso & elton muropa]
liwa ndomoyipi, ekuelingaa, eyi-elinga, golongani nanga
liwabi khumba-khumba, eyi-elinga, eyi-elinga, golongani nanga
(al!ck)
[verse 5: al!ck macheso]
impfa nimulandi anzanga, inandilanda, inandilanda
kundilanga mwana w-nga, omwe ndinabala kundisiya nandilira amayo
anzanga impfa nimulandi, inandilanda, inandilanda
kundlianga munzanga w-nga, -n-li wachikondi
kundisiya chocho
impfa nimulandi amayo, nimulandi ndikawalala
kutilanda makolo athu, omwe anatibala, kutisiya natilira atatee
chabwino makolo athu, mupume muntendere, (k-mwamba muliko mkomwe mukonze malo athu iiyii-yii-yii oooh-aaah!)
chabwino amayi anga mupume muntendere, (k-mwamba muliko amayo mukonze malo anga iiyii-yii-yii oooh-aaah!)

[verse 6]
[?]

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...