letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de mtima - achina gattah ase

Loading...

[chorus: piksy]
ndikagokuwona iwe
mtima w-nga kugu-gunda
nkati ndikusiye pena
mtima w-nga kukufuna
nde ukangosekelera
stress umayifufuta
ukangoti umandikonda
mtima w-nga kutukula

[verse 1: achina gattah ase]
natuluka mu shop nsanagule
namufusa dzina sanatchule
ndiwe kamwana
maybe
nkona ndufuna ndikhale wako baby
watichani?
be my queen
zachamba eti
kodi mwabwela pa bimmer yi queen?
eya
nanga bwanji ufuna kundikweza njinga?
monse wayambila kunditchinga
koma number ndipatseko
ngati aircon iwe ndi machine a mphepo
nane chikondi ndiyeseko
tiye kunyanja tikapitidwe mphepo
umu ndi mene ndinapezela love yanga
five years sakutayitsa nthawi yanga
i don’t think it will end in tears
timayambana koma–
[chorus: piksy]
ndikagokuwona iwe
mtima w-nga kugu-gunda
nkati ndikusiye pena
mtima w-nga kukufuna
nde ukangosekelera
stress umayifufuta
ukangoti umandikonda
mtima w-nga kutukula

[verse 2: gwamba]
ukangoti “hey” ntima w-nga
usain bolt
ndekuti tsiku langa basi walipanga sort
ukangoti “bae” olo vep ndimapanga boycott
koma makape akuyesetsa kuti apeze fault
koma nkazi w-ngwiro, mm
sudziwa bwandiro, mm
look ndi nyatwa koma matama ndi zero, mm
with you in my life moyo kufewa ngati pillow
koma fans imathoka poti gwambizzle ndi hero
nde tadekha kaye imva izi dona
iwe ndi ine ndi limodzi mpaka imvi dona
ndakhala ndikusakasaka wa cv dona
pano ndakupeza nde tiye kwa ntiz dona
[chorus: piksy]
ndikagokuwona iwe
mtima w-nga kugu-gunda
nkati ndikusiye pena
mtima w-nga kukufuna
nde ukangosekelera
stress umayifufuta
ukangoti umandikonda
mtima w-nga kutukula
ndikagokuwona iwe
mtima w-nga kugu-gunda
nkati ndikusiye pena
mtima w-nga kukufuna
nde ukangosekelera
stress umayifufuta
ukangoti umandikonda
mtima w-nga kutukula

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...