letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

letra de nfana wa malawi - 6th mw

Loading...

[intro]
tabwera uzawone kwathu
(this one about)
tabwera uzawone kwathu
tabwera uzawone kwathu
ayo landie

[pre-chorus]
mfana wa malawi (mfana wa malawi)
ndichi mfana cha malawi (ona malawi)
tiye kwathu ku malawi (tiye kwathu ku malawi)
ukawone ku malawi (ukawone ku malawi)

[chorus]
tiye ku likoma ukadye nsomba zokoma
from lake malawi to [?]
livin’ lavida loca
tiye ku likoma ukadye nsomba zokoma
from lake malawi to [?]
livin’ lavida loca

[verse 1]
somewhere in africa, don’t say ndife alimika
mfana wa malawi anatsilika
ukamputa bonzo anachilika
njira zonse -n-loweza
ndichi mfana chodabwitsa
game chimayiwerenga
palibe zomupusitsa
mfana wa malawi spendin’ the money
sungamudutse osapeleka moni
amatha ku survivor olo ku joni
ama runner dancehall osawona mission
[pre-chorus]
mfana wa malawi
ndichi mfana cha malawi
tiye kwathu ku malawi
ukawone ku malawi

[chorus]
tiye ku likoma ukadye nsomba zokoma
from lake malawi to [?]
livin’ lavida loca
tiye ku likoma ukadyе nsomba zokoma
from lake malawi to [?]
livin’ lavida loca

[verse 2]
moni moni, muli bwanji achina eli njuchi?
kodi iwe big seh umamuziwa mandеm crispy?
joy nathu nayeso wathu
jay jay cee ndiwagulu lathu
onsewa ndi ana akwathu

[pre-chorus]
mfana wa malawi
ndichi mfana cha malawi
tiye kwathu ku malawi
ukawone ku malawi
[chorus]
tiye ku likoma ukadye nsomba zokoma
from lake malawi to [?]
livin’ lavida loca
tiye ku likoma ukadye nsomba zokoma
from lake malawi to [?]
livin’ lavida loca

letras aleatórias

MAIS ACESSADOS

Loading...