letras.top
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

iwe ndi ine - kay sadik

Loading...

(intro)

ooohwoouuoo woouuuwooo owoo
ooohwoouuoo woouuuwooo owoo
ohooo

[verse 1]

hunny…….
ndili ndi nkhani yoti
inu ndi ine…..tingomvana…..
ndine munthu ndimalakwisa….sindukana……
koma zomva imvazi ndima-dana nazo
zokamba kambazi ndima-kwiya nazooo
ngati pali vuto undidziwitse
usawuze wanthu atiyaluse
za ubale wathuwu sangathe (yeah)
ndati sangathe iwoowa (coz)
ndiwe wekha umandidziwa bho
ndine ndekha nmakudziwanso

[hook]

mdziko lonseli ndimafuna
iwe ndi ine, eeeh, iwe ndi iwe (mmmhu)
pazokoma zonsezi ndimakonda
iwe ndi ine, mmmm, iwe ndi ineyo (ooohoo)

[verse 2]
am so happy for us (for us)
chiko-ndi umandipatsa nchapamwamba
iwe ndi ine mpakampaka ukalamba uu
i love every moment that i spend with you
ndiwe fupa lama fupa anga
i’ll die for you, am here for you baby
zokhumba zanga ndiwe
zokonda zanga ndiweyoo

[hook]

mdziko lonseli ndimafuna
iwe ndi ine, eeeh, iwe ndi iwe (mmmhu)
pazokoma zonsezi ndimakonda
iwe ndi ine, mmmm, iwe ndi ineyo (ooohoo)

[verse 3]
dziko lingawawe bwanji, ine ndili ndi iweyo
tisalole wina apasule chikondi cha ifeyo
kuwala ngati ngelo iwe (nzakuveka velo inee)
kuwala ngati ngelo iwe (nzakuveka velo i swear)
uzipanga zisankho zakoo, osati zanzakooo
do what you feel is right (yeah)
kunama nama nama amanama
koma timamvana afana timakhwana
kunama nama nama amanama
koma timamvana ifeyo timakwa-anaaa
hook
mdziko lonseli ndimafuna
iwe ndi ine, eeeh, iwe ndi iwe (mmmhu)
pazokoma zonsezi ndimakonda
iwe ndi ine, mmmm, iwe ndi ineyo (ooohoo) x2

[outro]
yeeeh iii yeeeeh